Ekisodo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ana a Isiraeli anaberekana ndipo anachuluka m’dzikomo. Iwo anapitiriza kuchulukana ndi kukhala amphamvu koposa, moti anadzaza m’dzikomo.+ Numeri 26:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Amenewa ndiwo anali mabanja a Manase. Amuna onse owerengedwa m’mabanja awo analipo 52,700.+ Numeri 26:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Amenewa ndiwo anali mabanja a ana a Efuraimu.+ Amuna onse owerengedwa m’mabanja awo analipo 32,500. Awa anali ana aamuna a Yosefe ndi mabanja awo.+
7 Ana a Isiraeli anaberekana ndipo anachuluka m’dzikomo. Iwo anapitiriza kuchulukana ndi kukhala amphamvu koposa, moti anadzaza m’dzikomo.+
37 Amenewa ndiwo anali mabanja a ana a Efuraimu.+ Amuna onse owerengedwa m’mabanja awo analipo 32,500. Awa anali ana aamuna a Yosefe ndi mabanja awo.+