Genesis 32:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kenako munthuyo anati: “Dzina lako silikhalanso Yakobo, koma Isiraeli,*+ pakuti walimbana+ ndi Mulungu ndi anthu, ndipo potsirizira pake wapambana.” Yesaya 44:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Uyu adzati: “Ine ndine wa Yehova.”+ Uyo adzadzitcha dzina la Yakobo,+ ndipo wina adzalemba padzanja lake kuti: “Wa Yehova.” Munthu winanso adzadzipatsa dzina la Isiraeli.’+
28 Kenako munthuyo anati: “Dzina lako silikhalanso Yakobo, koma Isiraeli,*+ pakuti walimbana+ ndi Mulungu ndi anthu, ndipo potsirizira pake wapambana.”
5 Uyu adzati: “Ine ndine wa Yehova.”+ Uyo adzadzitcha dzina la Yakobo,+ ndipo wina adzalemba padzanja lake kuti: “Wa Yehova.” Munthu winanso adzadzipatsa dzina la Isiraeli.’+