Salimo 37:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yembekezera Yehova, ndi kusunga njira zake,+Ndipo adzakukweza kuti ulandire dziko lapansi.+Pamene oipa akuphedwa, iwe udzaona.+ Salimo 59:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mulungu amene wandisonyeza kukoma mtima kosatha ndidzaonana naye maso ndi maso.+Mulungu adzachititsa kuti ndione adani anga, adaniwo atagonja.+ Salimo 91:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Udzayang’ana ndi maso ako,+Ndipo udzaona anthu oipa akulandira chilango.+ Salimo 92:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Diso langa lidzayang’ana adani anga atagonja,+Makutu anga adzamva za anthu ondiukira, anthu ochita zoipa.
34 Yembekezera Yehova, ndi kusunga njira zake,+Ndipo adzakukweza kuti ulandire dziko lapansi.+Pamene oipa akuphedwa, iwe udzaona.+
10 Mulungu amene wandisonyeza kukoma mtima kosatha ndidzaonana naye maso ndi maso.+Mulungu adzachititsa kuti ndione adani anga, adaniwo atagonja.+
11 Diso langa lidzayang’ana adani anga atagonja,+Makutu anga adzamva za anthu ondiukira, anthu ochita zoipa.