Salimo 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Bwererani+ mudzapulumutse moyo wanga, inu Yehova.+Ndipulumutseni chifukwa cha kukoma mtima kwanu kosatha.+ Salimo 119:88 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 88 Ndisungeni wamoyo monga mwa kukoma mtima kwanu kosatha,+Kuti ndisunge zikumbutso zotuluka pakamwa panu.+
4 Bwererani+ mudzapulumutse moyo wanga, inu Yehova.+Ndipulumutseni chifukwa cha kukoma mtima kwanu kosatha.+
88 Ndisungeni wamoyo monga mwa kukoma mtima kwanu kosatha,+Kuti ndisunge zikumbutso zotuluka pakamwa panu.+