Salimo 119:88 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 88 Ndisungeni wamoyo monga mwa kukoma mtima kwanu kosatha,+Kuti ndisunge zikumbutso zotuluka pakamwa panu.+ Maliro 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa cha kukoma mtima kosatha+ kwa Yehova, ife sitinafafanizidwe,+ ndipo chifundo chake sichidzatha.+
88 Ndisungeni wamoyo monga mwa kukoma mtima kwanu kosatha,+Kuti ndisunge zikumbutso zotuluka pakamwa panu.+
22 Chifukwa cha kukoma mtima kosatha+ kwa Yehova, ife sitinafafanizidwe,+ ndipo chifundo chake sichidzatha.+