Salimo 37:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yembekezera Yehova, ndi kusunga njira zake,+Ndipo adzakukweza kuti ulandire dziko lapansi.+Pamene oipa akuphedwa, iwe udzaona.+ Salimo 91:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Udzayang’ana ndi maso ako,+Ndipo udzaona anthu oipa akulandira chilango.+ Salimo 112:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mtima wake sungagwedezeke,+ ndipo sadzachita mantha,+ע [ʽAʹyin]Pamapeto pake adzayang’ana adani ake atagonjetsedwa.+
34 Yembekezera Yehova, ndi kusunga njira zake,+Ndipo adzakukweza kuti ulandire dziko lapansi.+Pamene oipa akuphedwa, iwe udzaona.+
8 Mtima wake sungagwedezeke,+ ndipo sadzachita mantha,+ע [ʽAʹyin]Pamapeto pake adzayang’ana adani ake atagonjetsedwa.+