Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 9:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kuwonjezera pamenepo, ndidzafunsa za magazi anu. Ngati magazi anu akhetsedwa ndi chamoyo chilichonse, chamoyocho chiyenera kuphedwa, ndipo ngati moyo wa munthu wachotsedwa ndi munthu mnzake ndidzaufuna kuchokera kwa iye.+

  • Deuteronomo 32:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Kondwerani, mitundu inu, pamodzi ndi anthu ake,+

      Pakuti adzabwezera magazi a atumiki ake,+

      Ndipo adzabwezera chilango kwa adani ake,+

      Nadzaphimba machimo a dziko la anthu ake.”

  • 2 Mafumu 24:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 komanso chifukwa cha magazi osalakwa+ amene iye anakhetsa, moti anadzaza Yerusalemu ndi magazi osalakwa, ndipo Yehova sanalole kukhululuka.+

  • Yesaya 26:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pakuti taonani! Yehova akubwera kuchokera kumene amakhala kuti adzaimbe mlandu anthu okhala m’dzikoli.+ Magazi amene dzikoli linakhetsa lidzawaonetsa poyera,+ ndipo silidzabisanso anthu amene linapha.”+

  • Luka 11:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 N’chifukwa chake m’badwo uwu udzafunsidwa za magazi a aneneri,+ okhetsedwa kuchokera pamene dziko linakhazikika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena