Genesis 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo Mulungu anati: “N’chiyani chimene wachitachi? Tamvera tsono. Magazi a m’bale wako akundilirira munthaka.+ Salimo 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pofunafuna okhetsa magazi,+ iye adzakumbukira ndithu anthu osautsidwa.+Sadzaiwala ndithu kulira kwawo.+ Ezekieli 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti magazi amene mzindawo wakhetsa ali mkati mwake.+ Waika magaziwo pathanthwe losalala, pamalo oonekera. Mzindawo sunathire magaziwo pansi kuti uwakwirire ndi dothi.+ Luka 11:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 N’chifukwa chake m’badwo uwu udzafunsidwa za magazi a aneneri,+ okhetsedwa kuchokera pamene dziko linakhazikika.+ Chivumbulutso 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 pakuti iwo anakhetsa magazi a oyera ndi a aneneri.+ Ndipo inu mwawapatsa magazi+ kuti amwe, ndipo n’zowayenereradi.”+ Chivumbulutso 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mwa iye munapezeka magazi+ a aneneri,+ a oyera,+ ndi a onse amene anaphedwa padziko lapansi.”+
10 Pamenepo Mulungu anati: “N’chiyani chimene wachitachi? Tamvera tsono. Magazi a m’bale wako akundilirira munthaka.+
12 Pofunafuna okhetsa magazi,+ iye adzakumbukira ndithu anthu osautsidwa.+Sadzaiwala ndithu kulira kwawo.+
7 Pakuti magazi amene mzindawo wakhetsa ali mkati mwake.+ Waika magaziwo pathanthwe losalala, pamalo oonekera. Mzindawo sunathire magaziwo pansi kuti uwakwirire ndi dothi.+
50 N’chifukwa chake m’badwo uwu udzafunsidwa za magazi a aneneri,+ okhetsedwa kuchokera pamene dziko linakhazikika.+
6 pakuti iwo anakhetsa magazi a oyera ndi a aneneri.+ Ndipo inu mwawapatsa magazi+ kuti amwe, ndipo n’zowayenereradi.”+