Levitiko 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Munthu aliyense mwa ana a Isiraeli kapena mlendo amene akukhala pakati panu akapita kosaka nyama, ndipo wapha nyama kapena mbalame yololeka kudya, azithira magazi ake pansi+ ndi kuwafotsera ndi dothi.+ Deuteronomo 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma musadye magazi ake.+ Muziwathira panthaka ngati madzi.+ Yesaya 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti taonani! Yehova akubwera kuchokera kumene amakhala kuti adzaimbe mlandu anthu okhala m’dzikoli.+ Magazi amene dzikoli linakhetsa lidzawaonetsa poyera,+ ndipo silidzabisanso anthu amene linapha.”+
13 “‘Munthu aliyense mwa ana a Isiraeli kapena mlendo amene akukhala pakati panu akapita kosaka nyama, ndipo wapha nyama kapena mbalame yololeka kudya, azithira magazi ake pansi+ ndi kuwafotsera ndi dothi.+
21 Pakuti taonani! Yehova akubwera kuchokera kumene amakhala kuti adzaimbe mlandu anthu okhala m’dzikoli.+ Magazi amene dzikoli linakhetsa lidzawaonetsa poyera,+ ndipo silidzabisanso anthu amene linapha.”+