Ezekieli 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti magazi amene mzindawo wakhetsa ali mkati mwake.+ Waika magaziwo pathanthwe losalala, pamalo oonekera. Mzindawo sunathire magaziwo pansi kuti uwakwirire ndi dothi.+
7 Pakuti magazi amene mzindawo wakhetsa ali mkati mwake.+ Waika magaziwo pathanthwe losalala, pamalo oonekera. Mzindawo sunathire magaziwo pansi kuti uwakwirire ndi dothi.+