Deuteronomo 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma musadye magazi ake.+ Muziwathira panthaka ngati madzi.+ Deuteronomo 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma magazi ake okha usadye.+ Uziwathira pansi ngati madzi.+