Levitiko 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Munthu aliyense mwa ana a Isiraeli kapena mlendo amene akukhala pakati panu akapita kosaka nyama, ndipo wapha nyama kapena mbalame yololeka kudya, azithira magazi ake pansi+ ndi kuwafotsera ndi dothi.+ Deuteronomo 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma musadye magazi ake.+ Muziwathira panthaka ngati madzi.+
13 “‘Munthu aliyense mwa ana a Isiraeli kapena mlendo amene akukhala pakati panu akapita kosaka nyama, ndipo wapha nyama kapena mbalame yololeka kudya, azithira magazi ake pansi+ ndi kuwafotsera ndi dothi.+