Genesis 40:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakapita masiku atatu, Farao akutulutsa n’kukudula mutu. Adzakupachika pamtengo,+ ndipo mbalame zidzadya nyama yako ndithu.”+ Numeri 25:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Gwira onse amene akutsogolera anthuwo, uwaphe ndipo mitembo yawo uindandalike padzuwa pamaso pa Yehova.+ Uchite zimenezo kuti mkwiyo wa Yehova umene wayakira Aisiraeli uchoke.” Deuteronomo 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Pakakhala munthu amene wachita tchimo loyenera chiweruzo choti aphedwe, ndiyeno munthuyo waphedwa,+ ndipo wam’pachika pamtengo,+
19 Pakapita masiku atatu, Farao akutulutsa n’kukudula mutu. Adzakupachika pamtengo,+ ndipo mbalame zidzadya nyama yako ndithu.”+
4 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Gwira onse amene akutsogolera anthuwo, uwaphe ndipo mitembo yawo uindandalike padzuwa pamaso pa Yehova.+ Uchite zimenezo kuti mkwiyo wa Yehova umene wayakira Aisiraeli uchoke.”
22 “Pakakhala munthu amene wachita tchimo loyenera chiweruzo choti aphedwe, ndiyeno munthuyo waphedwa,+ ndipo wam’pachika pamtengo,+