Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 41:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Zimene anamasulirazo n’zimene zinachitikadi. Ineyo ndinabwezeretsedwa pa ntchito,+ koma mnzangayo anapachikidwa.”+

  • Deuteronomo 21:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “Pakakhala munthu amene wachita tchimo loyenera chiweruzo choti aphedwe, ndiyeno munthuyo waphedwa,+ ndipo wam’pachika pamtengo,+

  • Yoswa 8:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ndipo mfumu ya Ai+ anaipachika pamtengo mpaka madzulo.+ Koma dzuwa litatsala pang’ono kulowa, Yoswa analamula kuti achotse mtembo wa mfumuyo+ pamtengopo. Atauchotsa mtembowo anakauponya pachipata cha mzindawo, n’kuufotsera ndi mulu waukulu wa miyala, ndipo muluwo ulipo mpaka lero.

  • Yoswa 10:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Kenako Yoswa anawakantha ndi kuwapha. Atatero anawapachika pamitengo isanu, pomwe anakhalapo mpaka madzulo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena