Genesis 40:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma mkulu wa ophika mkate anam’pachika,+ monga mmene Yosefe anawauzira pomasulira maloto+ aja.
22 Koma mkulu wa ophika mkate anam’pachika,+ monga mmene Yosefe anawauzira pomasulira maloto+ aja.