Genesis 40:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo anamuyankha kuti: “Talota maloto, koma palibe wotimasulira malotowo.” Pamenepo Yosefe anawauza kuti: “Kodi Mulungu sindiye amamasulira?+ Tandifotokozerani malotowo.” Danieli 2:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Sikuti chinsinsi chimenechi chaululidwa kwa ine chifukwa chakuti ndine wanzeru kuposa munthu wina aliyense ayi,+ koma chaululidwa ndi cholinga chakuti ndikumasulireni malotowo mfumu, ndiponso kuti mudziwe maganizo a mumtima mwanu.+
8 Iwo anamuyankha kuti: “Talota maloto, koma palibe wotimasulira malotowo.” Pamenepo Yosefe anawauza kuti: “Kodi Mulungu sindiye amamasulira?+ Tandifotokozerani malotowo.”
30 Sikuti chinsinsi chimenechi chaululidwa kwa ine chifukwa chakuti ndine wanzeru kuposa munthu wina aliyense ayi,+ koma chaululidwa ndi cholinga chakuti ndikumasulireni malotowo mfumu, ndiponso kuti mudziwe maganizo a mumtima mwanu.+