Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 41:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pamenepo Yosefe anayankha Farao kuti: “Yemwe anene uthenga wokhudza moyo wa inu Farao ndi Mulungu osati ine.”+

  • Salimo 25:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ubwenzi wolimba ndi Yehova ndi wa anthu amene amamuopa,+

      Pangano lakenso ndi la anthu oterowo, ndipo iye amawadziwitsa panganolo.+

  • Danieli 2:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Koma kuli Mulungu kumwamba amene ndi Woulula zinsinsi,+ ndipo wakudziwitsani, inu Mfumu Nebukadinezara, zimene zidzachitike m’masiku otsiriza.+ Maloto anu ndi masomphenya amene munaona muli pabedi lanu ndi awa:

  • Danieli 2:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Zidzakhala choncho chifukwa munaona kuti mwala unadulidwa kuphiri koma osati ndi manja a munthu,+ ndipo unaphwanya chitsulo, mkuwa, dongo, siliva ndi golide.+ Inu mfumu, Mulungu Wamkulu+ wakudziwitsani zimene zidzachitike m’tsogolo.+ Maloto amenewa ndi odalirika ndipo kumasulira kwake ndi kokhulupirika.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena