Deuteronomo 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 mtembo wake usakhale pamtengopo usiku wonse,+ koma uzionetsetsa kuti wamuika m’manda tsiku lomwelo, chifukwa aliyense wopachikidwa pamtengo ndi wotembereredwa ndi Mulungu.+ Usaipitse nthaka yako imene Yehova Mulungu wako akukupatsa monga cholowa.+ Yoswa 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Dzuwa likulowa, Yoswa analamula kuti atsitse mafumuwo pamitengoyo+ n’kuwaponyera m’phanga limene anabisalamo lija, ndipo anthuwo anachitadi zimenezi. Kenako anaika miyala ikuluikulu pakhomo la phangalo, yomwe ilipobe mpaka lero.
23 mtembo wake usakhale pamtengopo usiku wonse,+ koma uzionetsetsa kuti wamuika m’manda tsiku lomwelo, chifukwa aliyense wopachikidwa pamtengo ndi wotembereredwa ndi Mulungu.+ Usaipitse nthaka yako imene Yehova Mulungu wako akukupatsa monga cholowa.+
27 Dzuwa likulowa, Yoswa analamula kuti atsitse mafumuwo pamitengoyo+ n’kuwaponyera m’phanga limene anabisalamo lija, ndipo anthuwo anachitadi zimenezi. Kenako anaika miyala ikuluikulu pakhomo la phangalo, yomwe ilipobe mpaka lero.