Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 17:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Iye anapitiriza kuuza Davide kuti: “Tangoyerekeza kubwera kuno, ndipereka mnofu wako kwa mbalame zam’mlengalenga ndi kwa zilombo zakutchire.”+

  • 2 Samueli 21:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma Rizipa mwana wamkazi wa Aya+ anatenga chiguduli+ ndi kuchiyala pamwala kuti azikhala pamenepo, kuyambira kuchiyambi kwa nyengo yokolola kufikira pamene mvula inagwa pamitemboyo kuchokera kumwamba.+ Iye sanalole mbalame+ zam’mlengalenga kutera pamitemboyo masana, ndipo usiku sanalole zilombo zakutchire+ kufikapo.

  • Yeremiya 16:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 ‘Iwo adzafa ndi matenda oopsa+ ndipo sadzawalira maliro+ kapena kuikidwa m’manda+ koma adzakhala ngati manyowa panthaka.+ Iwo adzafa ndi lupanga ndiponso njala yaikulu.+ Mitembo yawo idzakhala chakudya cha zolengedwa zouluka zam’mlengalenga ndi zilombo zakutchire.’+

  • Ezekieli 39:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Iwe udzafera m’mapiri a ku Isiraeli+ limodzi ndi magulu ako onse a asilikali ndi anthu a mitundu ina amene adzakhale nawe. Ndidzakuperekani kwa mbalame zodya nyama, mbalame zamitundumitundu ndi zilombo zakutchire kuti mukhale chakudya chawo.”’+

  • Chivumbulutso 19:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndinaonanso mngelo ataimirira padzuwa. Iye anafuula ndi mawu okweza kwa mbalame+ zonse zouluka chapafupi m’mlengalenga, kuti: “Bwerani kuno, dzasonkhaneni ku phwando lalikulu la Mulungu la chakudya chamadzulo,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena