-
Ezekieli 33:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 “Uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Pali ine Mulungu wamoyo, ndithu anthu amene ali m’malo owonongedwa adzaphedwa ndi lupanga.+ Munthu amene ali kutchire ndidzam’pereka kwa chilombo cholusa kuti akhale chakudya chake.+ Anthu amene ali m’malo otetezeka ndi m’mapanga+ adzafa ndi mliri.
-