Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 63:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Adzaphedwa ndi lupanga,+

      Adzakhala chakudya cha nkhandwe.+

  • Salimo 79:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Apereka mitembo ya atumiki anu kwa mbalame kuti chikhale chakudya chawo.+

      Matupi a okhulupirika anu awapereka kwa zilombo zakutchire.+

  • Ezekieli 29:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Iwe ndidzakutaya m’chipululu pamodzi ndi nsomba zonse za m’ngalande za Nailo.+ Udzagwera panthaka+ ndipo palibe amene adzakutenge kukakuika m’manda. Ndidzakupereka kwa zilombo zakutchire ndi zolengedwa zouluka kuti ukhale chakudya chawo.+

  • Ezekieli 39:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Koma kwa iwe mwana wa munthu, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Uza mbalame zamitundumitundu ndi zilombo zonse zakutchire+ kuti: “Sonkhanani mubwere kuno. Sonkhanani pamodzi kuzungulira nsembe yanga imene ndikukuperekerani. Imeneyi ndi nsembe yaikulu m’mapiri a ku Isiraeli.+ Mukabwera mudzadya nyama ndi kumwa magazi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena