Ekisodo 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zitatero nsomba za mumtsinje wa Nailo zinafa,+ ndipo mtsinje wa Nailo unayamba kununkha. Aiguputo sanathenso kumwa madzi a mumtsinje wa Nailo.+ M’dziko lonse la Iguputo munali magazi okhaokha.
21 Zitatero nsomba za mumtsinje wa Nailo zinafa,+ ndipo mtsinje wa Nailo unayamba kununkha. Aiguputo sanathenso kumwa madzi a mumtsinje wa Nailo.+ M’dziko lonse la Iguputo munali magazi okhaokha.