Salimo 105:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Anasandutsa madzi awo kukhala magazi,+Ndipo anapha nsomba zawo.+