Ekisodo 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nsomba zimene zili mumtsinje wa Nailo zifa,+ ndipo mtsinje wa Nailo ununkha,+ moti Aiguputo safunanso kumwa madzi ake.”’”+ Ekisodo 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako Aiguputo onse anayamba kukumba zitsime m’mphepete mwa mtsinje wa Nailo, kuti apeze madzi akumwa, chifukwa sakanatha kumwa madzi a mumtsinje wa Nailo.+
18 Nsomba zimene zili mumtsinje wa Nailo zifa,+ ndipo mtsinje wa Nailo ununkha,+ moti Aiguputo safunanso kumwa madzi ake.”’”+
24 Kenako Aiguputo onse anayamba kukumba zitsime m’mphepete mwa mtsinje wa Nailo, kuti apeze madzi akumwa, chifukwa sakanatha kumwa madzi a mumtsinje wa Nailo.+