Ezekieli 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwe ndidzakutaya m’chipululu pamodzi ndi nsomba zonse za m’ngalande za Nailo.+ Udzagwera panthaka+ ndipo palibe amene adzakutenge kukakuika m’manda. Ndidzakupereka kwa zilombo zakutchire ndi zolengedwa zouluka kuti ukhale chakudya chawo.+
5 Iwe ndidzakutaya m’chipululu pamodzi ndi nsomba zonse za m’ngalande za Nailo.+ Udzagwera panthaka+ ndipo palibe amene adzakutenge kukakuika m’manda. Ndidzakupereka kwa zilombo zakutchire ndi zolengedwa zouluka kuti ukhale chakudya chawo.+