Deuteronomo 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 iyenso* adzakupatsani mvula pa nthawi yake m’dziko lanu,+ mvula yoyambirira ndi mvula yomaliza,+ ndipo mudzakololadi mbewu zanu ndi kukhaladi ndi vinyo wotsekemera* komanso mafuta. Yeremiya 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mumtima mwawo sananene kuti: “Tsopano tiyeni tiope Yehova Mulungu wathu,+ amene amatigwetsera mvula. Amatigwetsera mvula yoyamba ndi yomalizira pa nyengo yake,+ ndipo amaonetsetsa kuti tili ndi milungu yoikidwiratu imene timakolola.”+
14 iyenso* adzakupatsani mvula pa nthawi yake m’dziko lanu,+ mvula yoyambirira ndi mvula yomaliza,+ ndipo mudzakololadi mbewu zanu ndi kukhaladi ndi vinyo wotsekemera* komanso mafuta.
24 Mumtima mwawo sananene kuti: “Tsopano tiyeni tiope Yehova Mulungu wathu,+ amene amatigwetsera mvula. Amatigwetsera mvula yoyamba ndi yomalizira pa nyengo yake,+ ndipo amaonetsetsa kuti tili ndi milungu yoikidwiratu imene timakolola.”+