Ezekieli 38:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘Ndidzamubweretsera lupanga m’madera anga onse a m’mapiri kuti limuwononge,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+ ‘Aliyense adzapha m’bale wake ndi lupanga.+
21 “‘Ndidzamubweretsera lupanga m’madera anga onse a m’mapiri kuti limuwononge,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+ ‘Aliyense adzapha m’bale wake ndi lupanga.+