Ezekieli 38:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 ‘Ndidzamuyambitsira nkhondo mʼmapiri anga onse kuti amuwononge,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. ‘Aliyense adzapha mʼbale wake ndi lupanga.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 38:21 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, tsa. 227 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 26
21 ‘Ndidzamuyambitsira nkhondo mʼmapiri anga onse kuti amuwononge,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. ‘Aliyense adzapha mʼbale wake ndi lupanga.+