Ekisodo 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mogwirizana ndi mawu ake, Yehova anachitadi zimenezi tsiku lotsatira, ndipo ziweto zamitundu yonse za Aiguputo zinayamba kufa,+ koma palibe chiweto ngakhale chimodzi cha ana a Isiraeli chimene chinafa.
6 Mogwirizana ndi mawu ake, Yehova anachitadi zimenezi tsiku lotsatira, ndipo ziweto zamitundu yonse za Aiguputo zinayamba kufa,+ koma palibe chiweto ngakhale chimodzi cha ana a Isiraeli chimene chinafa.