Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 9:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pofika pano ndikanatambasula kale dzanja langa ndi kukupha ndi mliri, iweyo ndi anthu ako, kukufafanizani padziko lapansi.+

  • Salimo 78:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Mkwiyo wake anaulambulira njira.+

      Sanawabweze kuwachotsa ku imfa.

      Ndipo anawapha ndi mliri.+

  • Ezekieli 14:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Zidzateronso ndikadzabweretsa ziweruzo zanga zinayi izi zowononga:+ lupanga, njala, zilombo zolusa zakutchire ndi mliri.+ Ndidzatumiza zimenezi mu Yerusalemu kuti zikaphemo anthu ndi ziweto.+

  • Amosi 4:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “‘Anthu inu ndinakutumizirani mliri wofanana ndi umene unachitika ku Iguputo.+ Ndinapha anyamata anu ndi lupanga+ ndipo mahatchi anu analandidwa.+ Ndinachititsa fungo lonunkha lotuluka m’misasa yanu kufika kumphuno zanu,+ koma inu simunabwerere kwa ine,’+ watero Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena