Salimo 105:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wakumbukira pangano lake mpaka kalekale,+Wakumbukira lonjezo limene anapereka ku mibadwo 1,000,+