Salimo 91:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Palibe tsoka limene lidzakugwera,+Ndipo ngakhale mliri sudzayandikira hema wako.+ Miyambo 1:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma munthu wondimvera adzakhala mwabata+ ndipo sadzasokonezeka chifukwa choopa tsoka.”+ Miyambo 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chilungamo chimateteza munthu amene sachita zopweteka ena,+ koma wochimwa amawonongedwa ndi zoipa.+
6 Chilungamo chimateteza munthu amene sachita zopweteka ena,+ koma wochimwa amawonongedwa ndi zoipa.+