Salimo 121:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova adzakuteteza ku masoka onse.+Iye adzateteza moyo wako.+ Miyambo 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Palibe chopweteka chimene chidzagwere wolungama,+ koma anthu oipa ndi amene tsoka lizidzangowagwera.+
21 Palibe chopweteka chimene chidzagwere wolungama,+ koma anthu oipa ndi amene tsoka lizidzangowagwera.+