Miyambo 1:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chotero adzadya zipatso za njira yawo,+ ndipo adzakhuta malangizo awo.+ Yesaya 48:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova wanena kuti, “Oipa alibe mtendere.”+ Habakuku 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwenso adzakumwetsa+ ndipo udzaonekera kuti ndiwe wosadulidwa.+ Udzakhuta zinthu zamanyazi m’malo mwa ulemerero.+ Chikho chochokera m’dzanja lamanja la Yehova chidzakupeza+ ndipo ulemerero wako udzasanduka manyazi.
16 Iwenso adzakumwetsa+ ndipo udzaonekera kuti ndiwe wosadulidwa.+ Udzakhuta zinthu zamanyazi m’malo mwa ulemerero.+ Chikho chochokera m’dzanja lamanja la Yehova chidzakupeza+ ndipo ulemerero wako udzasanduka manyazi.