Ezekieli 28:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Udzafa ngati anthu osadulidwa ndipo alendo ndi amene adzakuphe,+ ine ndanena,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.” Ezekieli 32:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Kodi ndiwe wosangalatsa kwambiri kuposa ndani?+ Tsikira kumanda ndipo uikidwa limodzi ndi anthu osadulidwa.’+
10 “‘Udzafa ngati anthu osadulidwa ndipo alendo ndi amene adzakuphe,+ ine ndanena,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
19 “‘Kodi ndiwe wosangalatsa kwambiri kuposa ndani?+ Tsikira kumanda ndipo uikidwa limodzi ndi anthu osadulidwa.’+