Ezekieli 28:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Udzafa ngati anthu osadulidwa ndipo alendo ndi amene adzakuphe,+ ine ndanena,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
10 “‘Udzafa ngati anthu osadulidwa ndipo alendo ndi amene adzakuphe,+ ine ndanena,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”