Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 75:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 M’dzanja la Yehova muli kapu.+

      Kapuyo yadzaza ndi vinyo wosakaniza ndi zokometsera ndipo akuchita thovu.

      Ndithudi, iye adzatsanula vinyo yense amene ali m’kapuyo kuphatikizapo nsenga zake.

      Anthu onse oipa padziko lapansi adzamwa ndi kugugudiza nsengazo.”+

  • Yesaya 51:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ambuye wako, Yehova, Mulungu wako, amene amateteza+ anthu ake, wanena kuti: “Taona! Ine ndidzachotsa m’manja mwako chikho chochititsa munthu kudzandira.+ Sudzamwanso chipanda, chikho cha mkwiyo wanga.+

  • Yeremiya 51:57
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 57 Ndidzaledzeretsa akalonga, anthu ake anzeru, abwanamkubwa ake, atsogoleri ake ndi anthu ake amphamvu.+ Adzagona tulo tomwe tidzakhalapo mpaka kalekale ndipo sadzadzukanso,”+ yatero Mfumu,+ imene dzina lake ndi Yehova wa makamu.+

  • Chivumbulutso 18:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 M’bwezereni monga mmene iye anachitira.+ M’chitireni mowirikiza kawiri. Ndithu, wirikizani kawiri zinthu zimene iyeyo anachita.+ M’kapu+ imene anaikamo chakumwa chosakaniza, ikanimo chakumwa chakecho+ kuwirikiza kawiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena