Yobu 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu nawonso amagona pansi osadzuka.+Sadzadzuka mpaka kumwamba kutachoka,+Sadzadzutsidwa ku tulo tawo.+ Yeremiya 51:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “Chilakolako chawo chikadzakhala champhavu kwambiri ndidzawakonzera mapwando ndipo ndidzawaledzeretsa kuti asangalale.+ Pamenepo adzagona tulo tomwe tidzakhalapo mpaka kalekale, ndipo sadzadzukanso,”+ watero Yehova.
12 Anthu nawonso amagona pansi osadzuka.+Sadzadzuka mpaka kumwamba kutachoka,+Sadzadzutsidwa ku tulo tawo.+
39 “Chilakolako chawo chikadzakhala champhavu kwambiri ndidzawakonzera mapwando ndipo ndidzawaledzeretsa kuti asangalale.+ Pamenepo adzagona tulo tomwe tidzakhalapo mpaka kalekale, ndipo sadzadzukanso,”+ watero Yehova.