Yobu 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Maso ake adzaona kuwola kwake,Ndipo iye adzamwa mkwiyo wa Wamphamvuyonse.+ Salimo 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzavumbitsira oipa misampha, moto ndi sulufule,+Komanso mphepo yotentha, monga gawo limene ayenera kumwa.+ Yeremiya 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova Mulungu wa Isiraeli anandiuza kuti: “Landira chikho ichi chimene chili m’dzanja langa. Mmenemu muli vinyo wa mkwiyo ndipo ukamwetse mitundu yonse imene ndikukutumizako.+ Yeremiya 25:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ngati angakakane kulandira chikhochi m’manja mwako kuti amwe ukawauze kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Mumwabe basi.+
6 Iye adzavumbitsira oipa misampha, moto ndi sulufule,+Komanso mphepo yotentha, monga gawo limene ayenera kumwa.+
15 Yehova Mulungu wa Isiraeli anandiuza kuti: “Landira chikho ichi chimene chili m’dzanja langa. Mmenemu muli vinyo wa mkwiyo ndipo ukamwetse mitundu yonse imene ndikukutumizako.+
28 Ngati angakakane kulandira chikhochi m’manja mwako kuti amwe ukawauze kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Mumwabe basi.+