Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 21:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Maso ake adzaona kuwola kwake,

      Ndipo iye adzamwa mkwiyo wa Wamphamvuyonse.+

  • Salimo 75:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 M’dzanja la Yehova muli kapu.+

      Kapuyo yadzaza ndi vinyo wosakaniza ndi zokometsera ndipo akuchita thovu.

      Ndithudi, iye adzatsanula vinyo yense amene ali m’kapuyo kuphatikizapo nsenga zake.

      Anthu onse oipa padziko lapansi adzamwa ndi kugugudiza nsengazo.”+

  • Yesaya 51:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Dzuka! Dzuka! Imirira iwe Yerusalemu,+ iwe amene wamwa chikho cha mkwiyo wa Yehova kuchokera m’dzanja lake.+ Iweyo wamwa ndipo wagugudiza chipanda, chikho chochititsa munthu kuyenda dzandidzandi.+

  • Yeremiya 25:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 mafumu onse akumpoto, akutali ndi apafupi, mmodzi ndi mmodzi wa iwo, ndipo ndinamwetsanso maufumu ena onse a padziko lapansi. Mfumu ya Sesaki+ nayonso idzamwa pambuyo pa onsewa.

  • Chivumbulutso 14:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 adzamwanso vinyo wosasungunula wa mkwiyo+ wa Mulungu amene akuthiridwa m’kapu ya mkwiyo wake. Ndipo adzazunzidwa+ ndi moto ndi sulufule+ pamaso pa angelo oyera, ndi pamaso pa Mwanawankhosa.

  • Chivumbulutso 16:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Pamenepo mzinda waukulu+ unagawika zigawo zitatu, ndipo mizinda ya mitundu ya anthu inagwa. Ndiyeno Mulungu anakumbukira Babulo Wamkulu,+ kuti amupatse kapu yokhala ndi vinyo wa mkwiyo wake waukulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena