Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 87:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Yehova amakonda kwambiri zipata za Ziyoni+

      Kusiyana ndi mahema onse a Yakobo.+

  • Yesaya 32:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Anthu anga adzakhala pamalo amtendere ndi pamalo otetezeka. Adzakhala m’malo abata ndiponso aphee!+

  • Yesaya 33:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Taonani Ziyoni,+ tauni yathu yochitiramo zikondwerero.+ Maso anu adzaona Yerusalemu, amene ndi malo okhala aphee, opanda chosokoneza chilichonse. Iye ndi hema woti palibe amene adzamuchotse.+ Zikhomo zake sizidzazulidwa ndipo zingwe zake sizidzaduka.+

  • Yesaya 37:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 ‘Ndithu ndidzateteza+ mzinda uno kuti ndiupulumutse chifukwa cha ine mwini+ ndiponso chifukwa cha Davide mtumiki wanga.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena