2 Mafumu 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndithu ndiwonjezera zaka 15 pa masiku ako, ndipo ndidzalanditsa+ iweyo ndi mzindawu m’manja mwa mfumu ya Asuri. Ndidzateteza mzinda uno chifukwa cha ine mwini ndiponso chifukwa cha Davide mtumiki wanga.”’”+ Yesaya 31:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Monga imachitira mbalame imene ikuuluka kuti iteteze ana ake, Yehova wa makamu adzateteza mzinda wa Yerusalemu.+ Iye adzauteteza n’kuupulumutsa.+ Adzausunga n’kuuthandiza kuti upulumuke.” Yesaya 38:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzalanditsa iweyo ndi mzindawu m’manja mwa mfumu ya Asuri, ndipo ndidzateteza mzinda uno.+
6 Ndithu ndiwonjezera zaka 15 pa masiku ako, ndipo ndidzalanditsa+ iweyo ndi mzindawu m’manja mwa mfumu ya Asuri. Ndidzateteza mzinda uno chifukwa cha ine mwini ndiponso chifukwa cha Davide mtumiki wanga.”’”+
5 Monga imachitira mbalame imene ikuuluka kuti iteteze ana ake, Yehova wa makamu adzateteza mzinda wa Yerusalemu.+ Iye adzauteteza n’kuupulumutsa.+ Adzausunga n’kuuthandiza kuti upulumuke.”