Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 19:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 ‘Inu munaona nokha zimene ndinachitira Aiguputo,+ kuti ndikunyamuleni pamapiko a chiwombankhanga ndi kukubweretsani kwa ine.+

  • Deuteronomo 32:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Monga mmene chiwombankhanga chimagwedezera mwamphamvu chisa chake,

      Mmene chimaulukira pamwamba pa ana ake,+

      Mmene chimatambasulira mapiko ake, ndi kutenga anawo,

      N’kuwanyamula pamapiko ake,+

  • Salimo 91:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Adzakutchinjiriza ndi mapiko ake,+

      Udzathawira pansi pa mapiko ake.+

      Choonadi chake+ chidzakhala chishango chako+ chachikulu ndi malo ako achitetezo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena