-
Deuteronomo 32:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Monga mmene chiwombankhanga chimagwedezera mwamphamvu chisa chake,
Mmene chimaulukira pamwamba pa ana ake,+
Mmene chimatambasulira mapiko ake, ndi kutenga anawo,
N’kuwanyamula pamapiko ake,+
-