Yesaya 31:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Monga imachitira mbalame imene ikuuluka kuti iteteze ana ake, Yehova wa makamu adzateteza mzinda wa Yerusalemu.+ Iye adzauteteza n’kuupulumutsa.+ Adzausunga n’kuuthandiza kuti upulumuke.”
5 Monga imachitira mbalame imene ikuuluka kuti iteteze ana ake, Yehova wa makamu adzateteza mzinda wa Yerusalemu.+ Iye adzauteteza n’kuupulumutsa.+ Adzausunga n’kuuthandiza kuti upulumuke.”