Yesaya 31:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mofanana ndi mbalame imene imauluka kuti iteteze ana ake, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzateteza mzinda wa Yerusalemu.+ Iye adzauteteza nʼkuupulumutsa. Adzaonetsetsa kuti usawonongedwe ndipo adzaulanditsa.” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:5 Yesaya 1, tsa. 323 Nsanja ya Olonda,7/15/1996, tsa. 32
5 Mofanana ndi mbalame imene imauluka kuti iteteze ana ake, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzateteza mzinda wa Yerusalemu.+ Iye adzauteteza nʼkuupulumutsa. Adzaonetsetsa kuti usawonongedwe ndipo adzaulanditsa.”