Yesaya 31:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Monga imachitira mbalame imene ikuuluka kuti iteteze ana ake, Yehova wa makamu adzateteza mzinda wa Yerusalemu.+ Iye adzauteteza n’kuupulumutsa.+ Adzausunga n’kuuthandiza kuti upulumuke.” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:5 Yesaya 1, tsa. 323 Nsanja ya Olonda,7/15/1996, tsa. 32
5 Monga imachitira mbalame imene ikuuluka kuti iteteze ana ake, Yehova wa makamu adzateteza mzinda wa Yerusalemu.+ Iye adzauteteza n’kuupulumutsa.+ Adzausunga n’kuuthandiza kuti upulumuke.”