Ekisodo 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ‘Inu munaona nokha zimene ndinachitira Aiguputo,+ kuti ndikunyamuleni pamapiko a chiwombankhanga nʼkukubweretsani kwa ine.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:4 Yandikirani, ptsa. 67-68 Nsanja ya Olonda,6/15/1996, tsa. 11
4 ‘Inu munaona nokha zimene ndinachitira Aiguputo,+ kuti ndikunyamuleni pamapiko a chiwombankhanga nʼkukubweretsani kwa ine.+