Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 15:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Chifukwa cha kukhulupirika kwa Davide,+ Yehova Mulungu wake anam’patsa nyale+ mu Yerusalemu mwa kukweza mwana wake pambuyo pake, ndiponso kuchititsa kuti Yerusalemu akhalepobe.+

  • 2 Mafumu 19:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Ndithu ndidzateteza+ mzinda uno kuti ndiupulumutse chifukwa cha ine mwini+ ndiponso chifukwa cha Davide mtumiki wanga.”’”+

  • Yeremiya 30:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Inu mudzatumikira Yehova Mulungu wanu ndi Davide mfumu yanu+ imene ndidzakuutsirani.”+

  • Ezekieli 37:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 “‘“Mtumiki wanga Davide adzakhala mfumu yawo.+ Onse adzakhala ndi m’busa mmodzi.+ Iwo adzayenda motsatira zigamulo zanga+ ndipo adzasunga malamulo anga+ ndi kuwatsatira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena