Yesaya 55:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tcherani khutu+ lanu ndipo bwerani kwa ine.+ Mvetserani ndipo mudzakhalabe ndi moyo.+ Ine ndidzachita nanu pangano lokhalapo mpaka kalekale+ lokhudza kukoma mtima kwanga kosatha kosonyezedwa kwa Davide, kumene kuli kokhulupirika.+ Ezekieli 34:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzazipatsa m’busa mmodzi,+ amene ndi mtumiki wanga Davide,+ ndipo adzazidyetsa. Iye adzakhala m’busa wawo ndipo adzazidyetsadi.+ Hoseya 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako ana a Isiraeli adzabwerera ndi kufunafuna Yehova Mulungu wawo+ ndiponso Davide mfumu yawo.+ Iwo adzabwera kwa Yehova akunjenjemera+ ndipo adzafunafuna ubwino wake m’masiku otsiriza.+
3 Tcherani khutu+ lanu ndipo bwerani kwa ine.+ Mvetserani ndipo mudzakhalabe ndi moyo.+ Ine ndidzachita nanu pangano lokhalapo mpaka kalekale+ lokhudza kukoma mtima kwanga kosatha kosonyezedwa kwa Davide, kumene kuli kokhulupirika.+
23 Ndidzazipatsa m’busa mmodzi,+ amene ndi mtumiki wanga Davide,+ ndipo adzazidyetsa. Iye adzakhala m’busa wawo ndipo adzazidyetsadi.+
5 Kenako ana a Isiraeli adzabwerera ndi kufunafuna Yehova Mulungu wawo+ ndiponso Davide mfumu yawo.+ Iwo adzabwera kwa Yehova akunjenjemera+ ndipo adzafunafuna ubwino wake m’masiku otsiriza.+